Yohane 4:25-26

Yohane 4:25-26 CCL

Mayiyo anati, “Ine ndikudziwa kuti Mesiya (wotchedwa Khristu) akubwera. Akabwera, Iye adzafotokoza zonse kwa ife.” Ndipo Yesu anamuwuza kuti, “Amene ndikukuyankhulane, ndine amene.”