1
GENESIS 18:14
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Kodi chilipo chinthu chomkanika Yehova? Pa nthawi yoikidwa ndidzabwera kwa iwe, pakufika nyengo yake, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.
Compare
Explore GENESIS 18:14
2
GENESIS 18:12
ndipo Sara anaseka m'mtima mwake, nati, Kodi ndidzakhala ndi kukondwa ine nditakalamba, ndiponso mbuyanga ali wokalamba?
Explore GENESIS 18:12
3
GENESIS 18:18
Pakuti Abrahamu adzakhala ndithu wamkulu ndi wamphamvu, ndipo mitundu yonse ya dziko lapansi idzadalitsika mwa iye?
Explore GENESIS 18:18
4
GENESIS 18:23-24
Ndipo Abrahamu anayandikira nati, Kodi mudzaononga olungama pamodzi ndi oipa? Kapena alipo olungama makumi asanu m'kati mwa mudzi; kodi mudzaononga, simudzasiya malowo chifukwa cha olungama makumi asanu ali momwemo?
Explore GENESIS 18:23-24
5
GENESIS 18:26
Ndipo anati Yehova, Ndikapeza m'Sodomu olungama makumi asanu m'kati mwa mudzi, ndidzasiya malo onse chifukwa cha iwo.
Explore GENESIS 18:26
Home
Bible
Plans
Videos