1
LUKA 19:10
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pakuti Mwana wa Munthu anadza kufunafuna ndi kupulumutsa chotayikacho.
Compare
Explore LUKA 19:10
2
LUKA 19:38
nanena, Wolemekezeka Mfumuyo ikudza m'dzina la Ambuye; mtendere m'Mwamba, ndi ulemerero m'Mwambamwamba.
Explore LUKA 19:38
3
LUKA 19:9
Ndipo Yesu anati kwa iye, Lero chipulumutso chagwera nyumba iyi, popeza iyenso ndiye mwana wa Abrahamu.
Explore LUKA 19:9
4
LUKA 19:5-6
Ndipo m'mene anadza pamalopo Yesu anakweza maso nati kwa iye, Zakeyo, fulumira, nutsike; pakuti lero ndiyenera kukhala m'nyumba mwako. Ndipo anafulumira, natsika, namlandira Iye wokondwera.
Explore LUKA 19:5-6
5
LUKA 19:8
Ndipo Zakeyo anaimirira nati kwa Ambuye, Taonani, Ambuye, gawo limodzi la zanga zonse zogawika pakati ndipatsa osauka; ndipo ngati ndalanda kanthu kwa munthu monyenga, ndimbwezera kanai.
Explore LUKA 19:8
6
LUKA 19:39-40
Ndipo Afarisi ena a m'khamu la anthu anati kwa Iye, Mphunzitsi, dzudzulani ophunzira anu. Ndipo anayankha nati, Ndinena ndi inu, ngati awa khala chete miyala idzafuula.
Explore LUKA 19:39-40
Home
Bible
Plans
Videos