Yohane 19:36-37
Yohane 19:36-37 CCL
Zinthu izi zinachitika kuti malemba akwaniritsidwe: “Palibe limodzi la mafupa limene lidzathyoledwa,” ndi monga lemba linanso linena, “Iwo adzayangʼana Iye amene iwo anamubaya.”