MACHITIDWE A ATUMWI 4:31
MACHITIDWE A ATUMWI 4:31 BLPB2014
Ndipo m'mene adapemphera iwo, panagwedezeka pamalo pamene adasonkhanirapo; ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nalankhula mau a Mulungu molimbika mtima.