EKSODO 2:24-25
EKSODO 2:24-25 BLPB2014
Ndipo Mulungu anamva kubuula kwao, ndi Mulungu anakumbukira chipangano chake ndi Abrahamu, ndi Isaki, ndi Yakobo. Ndipo Mulungu anapenya Aisraele, ndi Mulungu anadziwa.