GENESIS 47:5-6
GENESIS 47:5-6 BLPB2014
Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Atate wako ndi abale ako afika kwa iwe; dziko la Ejipito lili pamaso pako: uwakhazike atate wako ndi abale ako pa dera lokometsetsa la dziko; akhale m'dziko la Goseni; ndipo ngati udziwa anthu anzeru a mwa iwo, uwaike iwo ayang'anire ng'ombe zanga.