LUKA 7:47-48
LUKA 7:47-48 BLPB2014
Chifukwa chake, ndinena kwa iwe, Machimo ake, ndiwo ambiri, akhululukidwa; chifukwa anakonda kwambiri; koma munthu amene anamkhululukira pang'ono, iye akonda pang'ono. Ndipo anati kwa mkazi, Machimo ako akhululukidwa.