YouVersion Logo
Search Icon

Kuyamba 25:23

Kuyamba 25:23 KUNDA

Chawuta adati kwayiye, “M'mimba mwako muna mishowo miwili, wanthu awili, wawun'zabala an'zakhala wakugawika. Munango an'zakhala wamphamvu kuposa munango, nkulu an'zatumikila mung'ono.”