1
YOHANE 20:21-22
Buku Lopatulika
BLP-2018
Chifukwa chake Yesu anatinso kwa iwo, Mtendere ukhale ndi inu; monga Atate wandituma Ine, Inenso ndituma inu. Ndipo pamene anati ichi anawapumira, nanena nao, Landirani Mzimu Woyera.
Compara
Explorar YOHANE 20:21-22
2
YOHANE 20:29
Yesu ananena kwa iye, Chifukwa wandiona Ine, wakhulupirira; odala iwo akukhulupirira, angakhale sanaone.
Explorar YOHANE 20:29
3
YOHANE 20:27-28
Pomwepo ananena kwa Tomasi, Bwera nacho chala chako kuno, nuone manja anga, ndipo bwera nalo dzanja lako, nuliike kunthiti yanga, ndipo usakhale wosakhulupirira, koma wokhulupirira. Tomasi anayankha nati kwa Iye, Ambuye wanga, ndi Mulungu wanga.
Explorar YOHANE 20:27-28
Inici
La Bíblia
Plans
Vídeos