1
LUKA 18:1
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo anawanenera fanizo lakuti ayenera iwo kupemphera nthawi zonse, osafooka mtima
Compara
Explorar LUKA 18:1
2
LUKA 18:7-8
Ndipo kodi Mulungu sadzachitira chilungamo osankhidwa ake akumuitana usana ndi usiku, popeza aleza nao mtima? Ndinena ndi inu, adzawachitira chilungamo posachedwa. Koma Mwana wa Munthu pakudza Iye, adzapeza chikhulupiriro pa dziko lapansi kodi?
Explorar LUKA 18:7-8
3
LUKA 18:27
Koma Iye anati, Zinthu zosatheka ndi anthu zitheka ndi Mulungu.
Explorar LUKA 18:27
4
LUKA 18:4-5
Ndipo sanafune nthawi; koma bwinobwino anati mwa yekha, Ndingakhale sindiopa Mulungu kapena kusamala munthu; koma chifukwa cha kundivuta ine mkazi wamasiye amene ndidzamweruzira mlandu, kuti angandilemetse ndi kudzaidza kwake.
Explorar LUKA 18:4-5
5
LUKA 18:17
Indetu ndinena kwa inu, Aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana, sadzalowamo ndithu.
Explorar LUKA 18:17
6
LUKA 18:16
Koma Yesu anawaitana, nanena, Lolani ana adze kwa Ine, ndipo musawaletse; pakuti Ufumu wa Mulungu uli wa otere.
Explorar LUKA 18:16
7
LUKA 18:42
Ndipo Yesu anati kwa iye, Penyanso: chikhulupiriro chako chakupulumutsa iwe.
Explorar LUKA 18:42
8
LUKA 18:19
Koma Yesu anati kwa iye, Unditcha Ine wabwino bwanji? Palibe wabwino, koma mmodzi, ndiye Mulungu.
Explorar LUKA 18:19
Inici
La Bíblia
Plans
Vídeos