Genesis 22:15-16

Genesis 22:15-16 CCL

Mngelo wa Yehova anayitana Abrahamu kuchokera kumwamba kachiwiri ndipo anati, “Ndikulumbira mwa Ine ndekha kuti popeza wachita zimenezi, wosandikaniza mwana wako mmodzi yekhayu