YOHANE 2:7-8

YOHANE 2:7-8 BLPB2014

Yesu ananena nao, Dzazani mitsukoyo ndi madzi. Naidzaza, ndendende. Ndipo ananena nao, Tungani tsopano, mupite nao kwa mkulu wa phwando. Ndipo anapita nao.