1
MARKO 15:34
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo pa ora lachisanu ndi chinai Yesu anafuula ndi mau okweza, Eloi, Eloi, lama sabakitani? ndiko kusandulika, Mulungu wanga, Mulungu wanga mwandisiyiranji Ine?
השווה
חקרו MARKO 15:34
2
MARKO 15:39
Ndipo pamene kenturiyo, woimirirapo popenyana ndi Iye, anaona kuti anapereka mzimu kotero, anati, Zoonadi, munthu uyu anali Mwana wa Mulungu.
חקרו MARKO 15:39
3
MARKO 15:38
Ndipo chinsalu chotchinga cha m'Kachisi chinang'ambika pakati, kuyambira kumwamba kufikira pansi.
חקרו MARKO 15:38
4
MARKO 15:37
Ndipo Yesu anatulutsa mau okweza, napereka mzimu wake.
חקרו MARKO 15:37
5
MARKO 15:33
Ndipo pofika ora lachisanu ndi chimodzi, panali mdima pa dziko lonse, kufikira ora lachisanu ndi chinai.
חקרו MARKO 15:33
6
MARKO 15:15
Ndipo Pilato pofuna kuwakhazika mtima anthuwo, anawamasulira Barabasi, napereka Yesu, atamkwapula, akampachike pamtanda.
חקרו MARKO 15:15
בית
כתבי הקודש
תוכניות
קטעי וידאו