MACHITIDWE A ATUMWI 10:34-35

MACHITIDWE A ATUMWI 10:34-35 BLPB2014

Ndipo Petro anatsegula pakamwa pake, nati, Zoona ndizindikira kuti Mulungu alibe tsankho; koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.