MACHITIDWE A ATUMWI 15:8-9

MACHITIDWE A ATUMWI 15:8-9 BLPB2014

Ndipo Mulungu, amene adziwa mtima, anawachitira umboni; nawapatsa Mzimu Woyera, monga anatipatsa ife; ndipo sanalekanitsa ife ndi iwo, nayeretsa mitima yao m'chikhulupiriro.