MACHITIDWE A ATUMWI 2:38

MACHITIDWE A ATUMWI 2:38 BLPB2014

Koma Petro anati kwa iwo, Lapani, batizidwani yense wa inu m'dzina la Yesu Khristu kuloza ku chikhululukiro cha machimo anu; ndipo mudzalandira mphatso ya Mzimu Woyera.