MACHITIDWE A ATUMWI 2:44-45

MACHITIDWE A ATUMWI 2:44-45 BLPB2014

Ndipo onse akukhulupirira anali pamodzi, nakhala nazo zonse zodyerana. Ndipo zimene anali nazo, ndi chuma chao, anazigulitsa, nazigawira kwa onse, monga momwe yense anasowera.