MACHITIDWE A ATUMWI 3:16

MACHITIDWE A ATUMWI 3:16 BLPB2014

Ndipo pa chikhulupiriro cha m'dzina lake dzina lakelo linalimbikitsa iye amene mumuona, nimumdziwa; ndipo chikhulupiriro chili mwa Iye chinampatsa kuchira konse kumeneku pamaso pa inu nonse.