1
Yoh. 4:24
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
Mulungu ndi mzimu, ndipo ompembedza Iye ayenera kumpembedza mwauzimu ndi moona.”
Linganisha
Chunguza Yoh. 4:24
2
Yoh. 4:23
Koma ikudza nthaŵi, ndipo yafika kale, pamene anthu opembedza kwenikweni adzapembedza Atate mwauzimu ndi moona. Atate amafuna anthu otere kuti ndiwo azimpembedza.
Chunguza Yoh. 4:23
3
Yoh. 4:14
Koma aliyense wodzamwa madzi amene Ine ndidzampatse, sadzamvanso ludzu konse mpaka muyaya. Madzi amene ndidzampatsewo azidzatumphukira mwa iye ngati kasupe wa madzi opatsa moyo, nkumupatsa moyo wosatha.”
Chunguza Yoh. 4:14
4
Yoh. 4:10
Yesu adati, “Mukadadziŵa mphatso ya Mulungu, mukadadziŵanso amene akupempha madzi akumwayu, bwenzi mutampempha ndi inuyo mai, Iye nakupatsani madzi opatsa moyo.”
Chunguza Yoh. 4:10
5
Yoh. 4:34
Koma Yesu adati, “Chakudya changa nkuchita zimene afuna Atate amene adandituma, kuti nditsirize ntchito imene Iwo adandipatsa.
Chunguza Yoh. 4:34
6
Yoh. 4:11
Maiyo adati, “Bambo, mulibe nchotungira chomwe, ndipo chitsimechi nchozama. Nanga madzi opatsa moyowo muŵatenga kuti?
Chunguza Yoh. 4:11
7
Yoh. 4:25-26
Maiyo adati, “Ndikudziŵa kuti akudza Mpulumutsi wolonjezedwa uja. Iyeyo akadzafika, adzatifotokozera zonse.” Yesu adamuuza kuti, “Ndine amene, Ineyo amene ndikulankhula nanu, mai.”
Chunguza Yoh. 4:25-26
8
Yoh. 4:29
“Tiyeni, mukaone munthu amene wandiwuza zonse zimene ine ndidachita. Kodi ameneyu sangakhale Mpulumutsi wolonjezedwa uja kapena?”
Chunguza Yoh. 4:29
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video