1
Yohane 13:34-35
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
“Lamulo latsopano limene ndikukupatsani ndi lakuti: Kondanani wina ndi mnzake, monga momwe Ine ndinakonda inu. Nanunso mukondane wina ndi mnzake. Mukamakondana aliyense adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga.”
Compare
Explore Yohane 13:34-35
2
Yohane 13:14-15
Tsono ngati Ine, Mbuye wanu ndi Mphunzitsi wanu, ndasambitsa mapazi anu, inunso muyenera kusambitsana mapazi anu. Ine ndakupatsani chitsanzo kuti muzichita monga Ine ndachitira.
Explore Yohane 13:14-15
3
Yohane 13:7
Yesu anayankha kuti, “Iwe sukuzindikira tsopano chimene ndikuchita, koma udzazindikira mʼtsogolo.”
Explore Yohane 13:7
4
Yohane 13:16
Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti wantchito saposa mbuye wake, kapena wotumidwa kuposa amene wamutuma.
Explore Yohane 13:16
5
Yohane 13:17
Ngati inu mudziwa zinthu zimenezi, mudzakhala odala mukamazichita.
Explore Yohane 13:17
6
Yohane 13:4-5
anayimirira kuchoka pa chakudya navula zovala zake natenga nsalu yopukutira nadzimanga mʼchiwuno mwake. Atachita izi, anathira madzi mʼbeseni ndi kuyamba kusambitsa mapazi a ophunzira ake, ndi kuwapukuta ndi chopukutira chimene anachimanga mʼchiwuno mwake.
Explore Yohane 13:4-5
Home
Bible
Plans
Videos