1
Yohane 20:21-22
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Yesu anatinso, “Mtendere ukhale nanu! Monga Atate anandituma Ine, Inenso ndikukutumani.” Ndi mawu amenewo Iye anawapumira ndipo anati, “Landirani Mzimu Woyera.
Compare
Explore Yohane 20:21-22
2
Yohane 20:29
Kenaka Yesu anamuwuza kuti, “Kodi wakhulupirira chifukwa wandiona Ine? Ndi odala amene amakhulupirira ngakhale asanaone.”
Explore Yohane 20:29
3
Yohane 20:27-28
Kenaka anati kwa Tomasi, “Ika chala chako apa; ona manja anga. Tambasula dzanja lako ndi kukhudza mʼnthiti mwanga. Leka kukayika, khulupirira.” Tomasi anati kwa Iye, “Ambuye wanga ndi Mulungu wanga!”
Explore Yohane 20:27-28
Home
Bible
Plans
Videos