1
Luka 23:34
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Yesu anati, “Atate, akhululukireni, pakuti sakudziwa chimene akuchita.” Ndipo anagawana malaya ake mochita maere.
Compare
Explore Luka 23:34
2
Luka 23:43
Yesu anayankha kuti, “Zoonadi, ndikukuwuza kuti lero lino udzakhala ndi Ine mʼparadaiso.”
Explore Luka 23:43
3
Luka 23:42
Kenaka anati, “Yesu, mundikumbukire ine pamene mulowa mu ufumu wanu.”
Explore Luka 23:42
4
Luka 23:46
Yesu anafuwula ndi mawu okweza kuti, “Atate, ndikupereka mzimu wanga mʼmanja mwanu.” Atanena zimenezi, anamwalira.
Explore Luka 23:46
5
Luka 23:33
Pamene anafika pamalo otchedwa Bade, anamupachika Iye pamodzi ndi achifwambawo, mmodzi kudzanja lake lamanja ndi winayo la ku lamazere.
Explore Luka 23:33
6
Luka 23:44-45
Linali tsopano pafupi ora lachisanu ndi chimodzi, ndipo mdima unagwa pa dziko lonse mpaka ora lachisanu ndi chinayi, pakuti dzuwa linaleka kuwala. Ndipo chinsalu cha mʼNyumba ya Mulungu chinangʼambika pakati.
Explore Luka 23:44-45
7
Luka 23:47
Kenturiyo, ataona zimene zinachitikazi, analemekeza Mulungu ndipo anati, “Zoonadi, uyu anali munthu wolungama.”
Explore Luka 23:47
Home
Bible
Plans
Videos