1
MARKO 14:36
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo ananena, Abba, Atate, zinthu zonse zitheka ndi Inu; mundichotsere chikho ichi; komatu si chimene ndifuna Ine, koma chimene mufuna Inu.
Compare
Explore MARKO 14:36
2
MARKO 14:38
Dikirani, pempherani, kuti mungalowe m'kuyesedwa; mzimutu uli wakufuna, koma thupi lili lolefuka.
Explore MARKO 14:38
3
MARKO 14:9
Ndipo ndithu ndinena ndi inu, Ponse pamene padzalalikidwa Uthenga Wabwino kudziko lonse lapansi, ichinso chimene anachita mkazi uyu chidzanenedwa, chikhale chonkumbukira nacho.
Explore MARKO 14:9
4
MARKO 14:34
Ndipo ananena nao, Moyo wanga uli wa chisoni chambiri, kufikira imfa. Bakhalani pano, nimundikire.
Explore MARKO 14:34
5
MARKO 14:22
Ndipo pamene iwo analikudya, Iye anatenga mkate, ndipo pamene anadalitsa, ananyema, napereka kwa iwo, kuti, Tengani; thupi langa ndi ili.
Explore MARKO 14:22
6
MARKO 14:23-24
Ndipo anatenga chikho, ndipo pamene adayamika, anapereka kwa iwo; ndipo iwo onse anamweramo. Ndipo Iye anati kwa iwo, Ichi ndi mwazi wanga wa chipangano, wothiridwa chifukwa cha anthu ambiri.
Explore MARKO 14:23-24
7
MARKO 14:27
Ndipo Yesu ananena nao, Mudzakhumudwa nonsenu; pakuti kwalembedwa, Ndidzakantha mbusa, ndi nkhosa zidzamwazika.
Explore MARKO 14:27
8
MARKO 14:42
Ukani, tizimuka; onani wakundiperekayo ali pafupi.
Explore MARKO 14:42
9
MARKO 14:30
Ndipo Yesu ananena naye, Ndithu ndinena ndi iwe, kuti lero, usiku uno, tambala asanalire kawiri, udzandikana Ine katatu.
Explore MARKO 14:30
Home
Bible
Plans
Videos