1
AROMA 7:25
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndiyamika Mulungu, mwa Yesu Khristu Ambuye wathu. Ndipo chotero ine ndekha ndi mtimatu nditumikira chilamulo cha Mulungu; koma ndi thupi nditumikira lamulo la uchimo.
Compare
Explore AROMA 7:25
2
AROMA 7:18
Pakuti ndidziwa kuti m'kati mwanga, ndiko m'thupi langa, simukhala chinthu chabwino; pakuti kufuna ndili nako, koma kuchita chabwino sindikupeza.
Explore AROMA 7:18
3
AROMA 7:19
Pakuti chabwino chimene ndichifuna, sindichichita; koma choipa chimene sindichifuna, chimenecho ndichichita.
Explore AROMA 7:19
4
AROMA 7:20
Koma ngati ndichita chimene sindichifuna, si ndinenso amene ndichichita, koma uchimo wakukhalabe m'kati mwanga ndiwo.
Explore AROMA 7:20
5
AROMA 7:21-22
Ndipo chotero ndipeza lamulo ili, kuti, pamene ndifuna chabwino, choipa chiliko. Pakuti monga mwa munthu wa m'kati mwanga, ine ndikondwera ndi chilamulo cha Mulungu
Explore AROMA 7:21-22
6
AROMA 7:16
Koma ngati ndichita chimene sindichifuna, ndivomerezana nacho chilamulo kuti chili chabwino.
Explore AROMA 7:16
Home
Bible
Plans
Videos