1
MACHITIDWE A ATUMWI 10:34-35
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo Petro anatsegula pakamwa pake, nati, Zoona ndizindikira kuti Mulungu alibe tsankho; koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.
השווה
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 10:34-35
2
MACHITIDWE A ATUMWI 10:43
Ameneyu aneneri onse amchitira umboni, kuti onse akumkhulupirira Iye adzalandira chikhululukiro cha machimo ao, mwa dzina lake.
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 10:43
בית
כתבי הקודש
תוכניות
קטעי וידאו