1
MACHITIDWE A ATUMWI 3:19
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Chifukwa chake lapani, bwererani kuti afafanizidwe machimo anu, kotero kuti zidze nyengo zakutsitsimutsa zochokera kunkhope ya Ambuye
השווה
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 3:19
2
MACHITIDWE A ATUMWI 3:6
Koma Petro anati, Siliva ndi golide ndilibe; koma chimene ndili nacho, ichi ndikupatsa, M'dzina la Yesu Khristu Mnazarayo, yenda.
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 3:6
3
MACHITIDWE A ATUMWI 3:7-8
Ndipo anamgwira iye kudzanja lake lamanja, namnyamutsa; ndipo pomwepo mapazi ake ndi mfundo za kumapazi zinalimbikitsidwa. Ndipo anazunzuka, naimirira, nayenda; ndipo analowa pamodzi nao m'Kachisi, nayenda, nalumpha, nayamika Mulungu.
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 3:7-8
4
MACHITIDWE A ATUMWI 3:16
Ndipo pa chikhulupiriro cha m'dzina lake dzina lakelo linalimbikitsa iye amene mumuona, nimumdziwa; ndipo chikhulupiriro chili mwa Iye chinampatsa kuchira konse kumeneku pamaso pa inu nonse.
חקרו MACHITIDWE A ATUMWI 3:16
בית
כתבי הקודש
תוכניות
קטעי וידאו