1
LUKA 24:49
Buku Lopatulika
Ndipo onani, Ine nditumiza pa inu lonjezano la Atate wanga; koma khalani inu m'mzinda muno, kufikira mwavekedwa ndi mphamvu yochokera Kumwamba.
Confronta
Esplora LUKA 24:49
2
LUKA 24:6
Palibe kuno Iye, komatu anauka; kumbukirani muja adalankhula nanu, pamene analinso mu Galileya
Esplora LUKA 24:6
3
LUKA 24:31-32
Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira Iye; ndipo anawakanganukira Iye, nawachokera. Ndipo anati wina kwa mnzake, Mtima wathu sunali wotentha m'kati mwathu nanga m'mene analankhula nafe m'njira, m'mene anatitsegulira malembo?
Esplora LUKA 24:31-32
4
LUKA 24:46-47
ndipo anati kwa iwo, Kotero kwalembedwa, kuti Khristu amve zowawa, nauke kwa akufa tsiku lachitatu; ndi kuti kulalikidwe m'dzina lake kulapa ndi kukhululukidwa kwa machimo kwa mitundu yonse, kuyambira ku Yerusalemu.
Esplora LUKA 24:46-47
5
LUKA 24:2-3
Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuuchotsa pamanda. Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.
Esplora LUKA 24:2-3
Home
Bibbia
Piani
Video