1
YOHANE 8:12
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pamenepo Yesu analankhulanso nao, nanena, Ine ndine kuunika kwa dziko lapansi; iye wonditsata Ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala nako kuunika kwa moyo.
Confronta
Esplora YOHANE 8:12
2
YOHANE 8:32
ndipo mudzazindikira choonadi, ndipo choonadi chidzakumasulani.
Esplora YOHANE 8:32
3
YOHANE 8:31
Chifukwa chake Yesu ananena kwa Ayuda aja adakhulupirira Iye, Ngati mukhala inu m'mau anga, muli ophunzira anga ndithu
Esplora YOHANE 8:31
4
YOHANE 8:36
Chifukwa chake ngati Mwana adzakuyesani inu aufulu, mudzakhala mfulu ndithu.
Esplora YOHANE 8:36
5
YOHANE 8:7
Koma pamene anakhalakhala alikumfunsabe Iye, anaweramuka, nati kwa iwo, Amene mwa inu ali wopanda tchimo, ayambe kumponya mwala.
Esplora YOHANE 8:7
6
YOHANE 8:34
Yesu anayankha iwo, nati, Indetu, indetu, ndinena kwa inu kuti yense wakuchita tchimo ali kapolo wa chimolo.
Esplora YOHANE 8:34
7
YOHANE 8:10-11
Koma Yesu pamene adaweramuka, anati kwa iye, Mkazi iwe, ali kuti ajawa? Palibe munthu anakutsutsa kodi? Koma iye anati, Palibe, Ambuye. Ndipo Yesu anati, Inenso sindikutsutsa iwe; pita; kuyambira tsopano usachimwenso.
Esplora YOHANE 8:10-11
Home
Bibbia
Piani
Video