Logo ya YouVersion
Elilingi ya Boluki

GENESIS 18:23-24

GENESIS 18:23-24 BLP-2018

Ndipo Abrahamu anayandikira nati, Kodi mudzaononga olungama pamodzi ndi oipa? Kapena alipo olungama makumi asanu m'kati mwa mzinda; kodi mudzaononga, simudzasiya malowo chifukwa cha olungama makumi asanu ali momwemo?