Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

GENESIS 1:29

GENESIS 1:29 BLP-2018

Ndipo anati Mulungu, Taonani, ndakupatsani inu therere lonse lakubala mbeu lili padziko lapansi, ndi mitengo yonse m'mene muli chipatso cha mtengo wakubala mbeu; chidzakhala chakudya cha inu