1
MACHITIDWE 4:12
Buku Lopatulika
Ndipo palibe chipulumutso mwa wina yense, pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo la kumwamba, lopatsidwa mwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
So sánh
Khám phá MACHITIDWE 4:12
2
MACHITIDWE 4:31
Ndipo m'mene adapemphera iwo, panagwedezeka pamalo pamene adasonkhanirapo; ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nalankhula mau a Mulungu molimbika mtima.
Khám phá MACHITIDWE 4:31
3
MACHITIDWE 4:29
Ndipo tsopano Ambuye, penyani mau ao akuopsa, ndipo patsani kwa akapolo anu alankhule mau anu ndi kulimbika mtima konse
Khám phá MACHITIDWE 4:29
4
MACHITIDWE 4:11
Iye ndiye mwalawo woyesedwa wopanda pake ndi inu omanga nyumba, umene unayesedwa mutu wa pangodya.
Khám phá MACHITIDWE 4:11
5
MACHITIDWE 4:13
Koma pakuona kulimbika mtima kwa Petro ndi Yohane, ndipo pozindikira kuti ndiwo anthu osaphunzira ndi opulukira, anazizwa ndipo anawazindikira, kuti adakhala pamodzi ndi Yesu.
Khám phá MACHITIDWE 4:13
6
MACHITIDWE 4:32
Ndipo unyinji wa iwo akukhulupirira anali wa mtima umodzi ndi moyo umodzi; ndipo sananene mmodzi kuti kanthu ka chuma anali nacho ndi kake ka iye yekha; koma anali nazo zonse zodyerana.
Khám phá MACHITIDWE 4:32
Trang chủ
Kinh Thánh
Kế hoạch
Video