1
MACHITIDWE 3:19
Buku Lopatulika
Chifukwa chake lapani, bwererani kuti afafanizidwe machimo anu, kotero kuti zidze nyengo zakutsitsimutsa zochokera kunkhope ya Ambuye
So sánh
Khám phá MACHITIDWE 3:19
2
MACHITIDWE 3:6
Koma Petro anati, Siliva ndi golide ndilibe; koma chimene ndili nacho, ichi ndikupatsa, M'dzina la Yesu Khristu Mnazarayo, yenda.
Khám phá MACHITIDWE 3:6
3
MACHITIDWE 3:7-8
Ndipo anamgwira iye kudzanja lake lamanja, namnyamutsa; ndipo pomwepo mapazi ake ndi mfundo za kumapazi zinalimbikitsidwa. Ndipo anazunzuka, naimirira, nayenda; ndipo analowa pamodzi nao mu Kachisi, nayenda, nalumpha, nayamika Mulungu.
Khám phá MACHITIDWE 3:7-8
4
MACHITIDWE 3:16
Ndipo pa chikhulupiriro cha m'dzina lake dzina lakelo linalimbikitsa iye amene mumuona, nimumdziwa; ndipo chikhulupiriro chili mwa Iye chinampatsa kuchira konse kumeneku pamaso pa inu nonse.
Khám phá MACHITIDWE 3:16
Trang chủ
Kinh Thánh
Kế hoạch
Video