1
LUKA 11:13
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Potero, ngati inu, okhala oipa, mudziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, koposa kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa Mzimu Woyera kwa iwo akumpempha Iye?
对照
探索 LUKA 11:13
2
LUKA 11:9
Ndipo Ine ndinena ndi inu, Pemphani, ndipo adzakupatsani; funani, ndipo mudzapeza; gogodani ndipo adzakutsegulirani.
探索 LUKA 11:9
3
LUKA 11:10
Pakuti yense wakupempha alandira; ndi wofuna apeza; ndi iye amene agogoda adzamtsegulira.
探索 LUKA 11:10
4
LUKA 11:2
Ndipo anati kwa iwo, M'mene mupemphera nenani, Atate, Dzina lanu liyeretsedwa; Ufumu wanu udze
探索 LUKA 11:2
5
LUKA 11:4
Ndipo mutikhululukire ife machimo athu; pakuti ifenso tikhululukira munthu yense wa mangawa athu. Ndipo musatitengere ife kokatiyesa.
探索 LUKA 11:4
6
LUKA 11:3
tipatseni ife tsiku ndi tsiku chakudya cha patsiku.
探索 LUKA 11:3
7
LUKA 11:34
Nyali ya thupi ndiyo diso lako; pamene paliponse diso lako lili langwiro thupi lako lonse liunikidwanso monsemo; koma likakhala loipa, thupi lako lomwe lili la mdima wokhawokha.
探索 LUKA 11:34
8
LUKA 11:33
Palibe munthu, atayatsa nyali, aiika m'chipinda chapansi, kapena pansi pa mbiya, koma pa choikapo chake, kuti iwo akulowamo aone kuunika.
探索 LUKA 11:33
主页
圣经
计划
视频