LUKA 14:34-35

LUKA 14:34-35 BLPB2014

Kotero mchere uli wokoma; koma ngati mchere utasukuluka adzaukoleretsa ndi chiyani? Suyenera kuuthira pamunda kapena padzala, autaya kunja. Amene ali nao makutu akumva amve.