Logo YouVersion
Eicon Chwilio

LUKA 23:44-45

LUKA 23:44-45 BLP-2018

Ndipo ora lake pamenepo linali ngati lachisanu ndi chimodzi. Ndipo panali mdima padziko lonse kufikira ora lachisanu ndi chinai, ndipo dzuwa linada. Ndipo nsalu yotchinga ya mu Kachisi inang'ambika pakati.