Mufananidzo weYouVersion
Mucherechedzo Wekutsvaka

LUKA 14:28-30

LUKA 14:28-30 BLPB2014

Pakuti ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja yaitali, sathanga wakhala pansi, nawerengera mtengo wake, aone ngati ali nazo zakuimaliza? Kuti kungachitike, pamene atakhazika pansi miyala ya kumaziko ake, osakhoza kuimaliza anthu onse akuyang'ana adzayamba kumseka iye, ndi kunena kuti, Munthu uyu anayamba kumanga, koma sanathe kumaliza.